SlideShare a Scribd company logo
AONJEZI
MITUNDU YA AONJEZI
MITUNDU YA AONJEZI
• Awonjezi alipo mitundu ingapo motere:
a. Muonjezi wamchitidwe
b. Muonjezi wamaonekedwe
c. Muonjezi wamkhalidwe
d. Muonjezi wa nthawi
e. Muonjezi wa malo
f. Muonjezi wokana
g. Muonjezi wovomera
h. Muonjezi wotsindika
i. Muonjezi wokayika
MUONJEZI WAMCHITIDWE
• Amanena za momwe ntchito idachitikira, ikuchitikira komanso
idzachitikire. Muonjezi ameneyu amayankha mafunso awa:
motani? bwanji?
Zitsanzo
a. Mtsikanayu akuyimba mwanthetemya.
b. Amayi amavina bwino.
c. Ochimwa adzalira modandaula.
MUONJEZI WAMAONEKEDWE
• Amakamba za mneni nthawi zonse ndipo amayankha funso
lakuti motani?
Zitsanzo
a. Maluwa awa akuwoneka mobiriwira.
b. Nyembazo zinkaoneka modera.
c. Akuwoneka mopusa.
MUONJEZI WAMKHALIDWE
• Amasonyeza za mkhalidwe wa mmene ntchito yachitikira
m’chiganizo ndipo amayankha funso loti motani?
Zitsanzo
a. Msungwana uyu walandira mphatso yake mwaulemu.
b. Iye amalima mwaulesi.
MUONJEZI WA NTHAWI
• Amanena za nthawi yomwe ntchito idachitikira, yachitikira
ndipo idzachitikira. Iyeyu amayankha mafunso awa: liti? nthawi
yanji?
Zitsanzo
a. Abambo ndi amayi adzanyamuka Loweruka.
b. Tidayamba kulima mwezi watha.
c. Chimanga ichi achitenga lero.
MUONJEZI WA MALO
• Amanena komwe ntchito idachitikira, yachitikira komanso
idzachitikire ndipo amadziwika ndi aphatikiram’mbuyo awa: mu-,
m’-, pa-, ku-, kumasinde omwe amathandiza popanga aonjezi a
mtunduwu. Iwowa amayankha mafunso monga: kuti? muti? muti?
Zitsanzo
a. Tipita kumudzi.
b. Tenga manyowa m’khola la mbuzi.
c. Ikani zofundazo pamphasa.
MUONJEZI WOKANA
• Amasonyeza kuti ntchito siidachitike, siichitika kapena
siidzachitika.
Zitsanzo
a. Ayi, sanatenge.
b. Toto, sindingasenze mtolowu.
c. Iyayi, sindidzapita nawo.
MUONJEZI WOVOMERA
• Amasonyeza kuti ntchito idachitika, ikuchitika kapena
idzachitika.
Zitsanzo
a. Inde, wataya ndiwe.
b. Chabwino, ndikuperekezani.
c. Eya, chikhochi ndaswa ndine.
MUONJEZI WOTSINDIKA
• Amasonyeza kutsimikizira kuti ntchito yachitika mopitirira
muyeso.
Zitsanzo
a. Mwayi adamenyedwa kwambiri dzulo.
b. Abambowa adatithandiza kwabasi.
c. Iye wakwiya zedi chifukwa basi yamuthawa.
MUONJEZI WOKAYIKA
• Amasonyeza kusakhulupirira kuti ntchito ichitika.
Zitsanzo
a. Kapena iweyo upita nawo.
b. Mwanayo mwina akhoza mayeso.
c. Kaya, ngati angabwerenso.

More Related Content

What's hot

Amagama Week 04.pdf
Amagama Week 04.pdfAmagama Week 04.pdf
Amagama Week 04.pdf
Shaniquasthole
 
Sakhiwo selibito
Sakhiwo selibitoSakhiwo selibito
Sakhiwo selibito
MachaweDlamini1
 
Ppt adjectives - class 5
Ppt   adjectives - class 5Ppt   adjectives - class 5
Ppt adjectives - class 5
Anu N
 
Adverbs
AdverbsAdverbs
Adverbs
psidjain
 
Ukufingqa
UkufingqaUkufingqa
Sobito
SobitoSobito
Izindlelazesenzo2 170828135830
Izindlelazesenzo2 170828135830Izindlelazesenzo2 170828135830
Izindlelazesenzo2 170828135830
Colile Dlamini
 
Grace micro lesson2
Grace micro lesson2Grace micro lesson2
Grace micro lesson2
GraceNgobeni
 
Adjectives for Senses Lesson 17
Adjectives for Senses Lesson 17Adjectives for Senses Lesson 17
Adjectives for Senses Lesson 17
trn2allah
 
Mashala
MashalaMashala
Pandiwa
PandiwaPandiwa
Pandiwa
Rodenio Eyas
 
Sentence Patterns - Grammar Lesson for Grades 5 and 6
Sentence Patterns - Grammar Lesson for Grades 5 and 6Sentence Patterns - Grammar Lesson for Grades 5 and 6
Sentence Patterns - Grammar Lesson for Grades 5 and 6
Mr. Ronald Quileste, PhD
 
Adjective
AdjectiveAdjective
Adjective
Dr. Imran Khan
 
Abstract noun by blessie anne luis
Abstract noun by blessie anne luisAbstract noun by blessie anne luis
Abstract noun by blessie anne luis
Occidental mindoro state College
 
Incwadi Yobungani.pptx
Incwadi Yobungani.pptxIncwadi Yobungani.pptx
Incwadi Yobungani.pptx
Ntombikayise Gwala
 
bophelo bja mohu.pptx
bophelo bja mohu.pptxbophelo bja mohu.pptx
bophelo bja mohu.pptx
Amantle4
 
PANGHALIP PATULAD
PANGHALIP PATULADPANGHALIP PATULAD
PANGHALIP PATULAD
Johdener14
 
Prepositional Phrases PowerPoint
Prepositional Phrases PowerPointPrepositional Phrases PowerPoint
Prepositional Phrases PowerPoint
diana.koscik
 
SUBJECT AND PREDICATE
SUBJECT AND PREDICATESUBJECT AND PREDICATE
SUBJECT AND PREDICATE
Laarni Eguia
 

What's hot (20)

Amagama Week 04.pdf
Amagama Week 04.pdfAmagama Week 04.pdf
Amagama Week 04.pdf
 
Sakhiwo selibito
Sakhiwo selibitoSakhiwo selibito
Sakhiwo selibito
 
Ppt adjectives - class 5
Ppt   adjectives - class 5Ppt   adjectives - class 5
Ppt adjectives - class 5
 
Adverbs
AdverbsAdverbs
Adverbs
 
Ukufingqa
UkufingqaUkufingqa
Ukufingqa
 
Sobito
SobitoSobito
Sobito
 
Izindlelazesenzo2 170828135830
Izindlelazesenzo2 170828135830Izindlelazesenzo2 170828135830
Izindlelazesenzo2 170828135830
 
Grace micro lesson2
Grace micro lesson2Grace micro lesson2
Grace micro lesson2
 
Adjectives for Senses Lesson 17
Adjectives for Senses Lesson 17Adjectives for Senses Lesson 17
Adjectives for Senses Lesson 17
 
Mashala
MashalaMashala
Mashala
 
Pandiwa
PandiwaPandiwa
Pandiwa
 
Sentence Patterns - Grammar Lesson for Grades 5 and 6
Sentence Patterns - Grammar Lesson for Grades 5 and 6Sentence Patterns - Grammar Lesson for Grades 5 and 6
Sentence Patterns - Grammar Lesson for Grades 5 and 6
 
Adjective
AdjectiveAdjective
Adjective
 
Abstract noun by blessie anne luis
Abstract noun by blessie anne luisAbstract noun by blessie anne luis
Abstract noun by blessie anne luis
 
Incwadi Yobungani.pptx
Incwadi Yobungani.pptxIncwadi Yobungani.pptx
Incwadi Yobungani.pptx
 
ISIFUNDO isikhangisi (1) (1)
ISIFUNDO isikhangisi (1) (1)ISIFUNDO isikhangisi (1) (1)
ISIFUNDO isikhangisi (1) (1)
 
bophelo bja mohu.pptx
bophelo bja mohu.pptxbophelo bja mohu.pptx
bophelo bja mohu.pptx
 
PANGHALIP PATULAD
PANGHALIP PATULADPANGHALIP PATULAD
PANGHALIP PATULAD
 
Prepositional Phrases PowerPoint
Prepositional Phrases PowerPointPrepositional Phrases PowerPoint
Prepositional Phrases PowerPoint
 
SUBJECT AND PREDICATE
SUBJECT AND PREDICATESUBJECT AND PREDICATE
SUBJECT AND PREDICATE
 

Mitundu ya aonjezi

  • 2. MITUNDU YA AONJEZI • Awonjezi alipo mitundu ingapo motere: a. Muonjezi wamchitidwe b. Muonjezi wamaonekedwe c. Muonjezi wamkhalidwe d. Muonjezi wa nthawi e. Muonjezi wa malo f. Muonjezi wokana g. Muonjezi wovomera h. Muonjezi wotsindika i. Muonjezi wokayika
  • 3. MUONJEZI WAMCHITIDWE • Amanena za momwe ntchito idachitikira, ikuchitikira komanso idzachitikire. Muonjezi ameneyu amayankha mafunso awa: motani? bwanji? Zitsanzo a. Mtsikanayu akuyimba mwanthetemya. b. Amayi amavina bwino. c. Ochimwa adzalira modandaula.
  • 4. MUONJEZI WAMAONEKEDWE • Amakamba za mneni nthawi zonse ndipo amayankha funso lakuti motani? Zitsanzo a. Maluwa awa akuwoneka mobiriwira. b. Nyembazo zinkaoneka modera. c. Akuwoneka mopusa.
  • 5. MUONJEZI WAMKHALIDWE • Amasonyeza za mkhalidwe wa mmene ntchito yachitikira m’chiganizo ndipo amayankha funso loti motani? Zitsanzo a. Msungwana uyu walandira mphatso yake mwaulemu. b. Iye amalima mwaulesi.
  • 6. MUONJEZI WA NTHAWI • Amanena za nthawi yomwe ntchito idachitikira, yachitikira ndipo idzachitikira. Iyeyu amayankha mafunso awa: liti? nthawi yanji? Zitsanzo a. Abambo ndi amayi adzanyamuka Loweruka. b. Tidayamba kulima mwezi watha. c. Chimanga ichi achitenga lero.
  • 7. MUONJEZI WA MALO • Amanena komwe ntchito idachitikira, yachitikira komanso idzachitikire ndipo amadziwika ndi aphatikiram’mbuyo awa: mu-, m’-, pa-, ku-, kumasinde omwe amathandiza popanga aonjezi a mtunduwu. Iwowa amayankha mafunso monga: kuti? muti? muti? Zitsanzo a. Tipita kumudzi. b. Tenga manyowa m’khola la mbuzi. c. Ikani zofundazo pamphasa.
  • 8. MUONJEZI WOKANA • Amasonyeza kuti ntchito siidachitike, siichitika kapena siidzachitika. Zitsanzo a. Ayi, sanatenge. b. Toto, sindingasenze mtolowu. c. Iyayi, sindidzapita nawo.
  • 9. MUONJEZI WOVOMERA • Amasonyeza kuti ntchito idachitika, ikuchitika kapena idzachitika. Zitsanzo a. Inde, wataya ndiwe. b. Chabwino, ndikuperekezani. c. Eya, chikhochi ndaswa ndine.
  • 10. MUONJEZI WOTSINDIKA • Amasonyeza kutsimikizira kuti ntchito yachitika mopitirira muyeso. Zitsanzo a. Mwayi adamenyedwa kwambiri dzulo. b. Abambowa adatithandiza kwabasi. c. Iye wakwiya zedi chifukwa basi yamuthawa.
  • 11. MUONJEZI WOKAYIKA • Amasonyeza kusakhulupirira kuti ntchito ichitika. Zitsanzo a. Kapena iweyo upita nawo. b. Mwanayo mwina akhoza mayeso. c. Kaya, ngati angabwerenso.