SlideShare a Scribd company logo
Ntchito za maina
Kukhala mchitantchito (mwininkhani)
• Dzina limakhala mchitantchito ngati likugwira
ntchito m’chiganizo.
Zitsanzo
• Madalitso akuyendetsa galimoto.
• Abambo akulima.
Kukhala mchitidwantchito
(pamtherankhani)
• Dzina limakhala mchitidwantchito ngati
ntchito yachitikira pa ilo m’chiganizo. Mayina
omwe amakhala mchitidwantchito amagwira
ntchito zitatu zomwe ndi kukhala
mchitidwantchito wa chindunji, wopanda
chindunji ndi wamperekezi.
(a) Kukhala mchitidwantchito
wachindunji
• Dzina limakhala mchitidwantchito wachindunji
pamene ntchito ya mneni yachitikira pa ilo
molunjika.
Zitsanzo
• Mphatso akumweta udzu.
• Tikudya bwemba.
• Nasibeko waumba mphika.
(b) Kukhala mchitidwantchito
wopanda chindunji
• Dzina limakhala mchitidwantchito wopanda
chindunji pamene ntchito ya mneni
siinachitike pa ilo molunjika koma
langokhudzidwa chabe ndi ntchitoyo.
Zitsanzo
• Maliya walembera agogo kalata.
• Mphatso wagulira Mwayi pensulo.
(c) Kukhala mchitidwantchito wa
mperekezi
• Dzina limakhala mchitidwantchito wa
mperekezi pamene lili patsogolo pa mperekezi
m’chiganizo.
Zitsanzo
• Wandicheka ndi mpeni.
• Wapita kwa amalume.
Kukhala mtsirizitsi wa tanthauzo la
mneni
• Dzina limakhala mtsirizitsi wa tanthauzo la
mneni pamene likumalizitsa tanthauzo la
mneni kuti limveke bwino m’chiganizo.
Zitsanzo
• Mphunzitsiyo ndi katswiri.
• M’kalasi muli ophunzira ochepa.
Kukhala dzina loitanira
• Dzina limakhala loitanira pamene likusonyeza
za yemwe akuitanidwa pa nthawiyo.
Zitsanzo
• Chifundo, bwera kuno.
• Ananu, pitani kunyumba

More Related Content

What's hot

2D and 3D shapes and describe their properties ppt.pptx
2D and 3D shapes and describe their properties ppt.pptx2D and 3D shapes and describe their properties ppt.pptx
2D and 3D shapes and describe their properties ppt.pptx
JennySinaga1
 
Calculating speed time and distance
Calculating speed time and distanceCalculating speed time and distance
Calculating speed time and distance
NeilfieOrit2
 
Integers Class 7
Integers Class 7 Integers Class 7
Integers Class 7
JiyaWalia
 
Lines and angles
Lines and anglesLines and angles
Lines and angles
Mohammed Nehan
 
Area of a triangle
Area of a triangleArea of a triangle
Area of a triangle
Aileen Alorro
 
Square Roots And Perfect Squares
Square Roots And Perfect SquaresSquare Roots And Perfect Squares
Square Roots And Perfect Squares
veggie189
 
Visualising solid shapes
Visualising solid shapesVisualising solid shapes
Visualising solid shapes
Tirth Dave
 
Area of rectangles
Area of rectanglesArea of rectangles
Area of rectanglesWorserbay
 
Area of quadrilaterals
Area of quadrilateralsArea of quadrilaterals
Area of quadrilaterals
Nisha Neethu
 
triangle and its properties
triangle and its propertiestriangle and its properties
triangle and its properties
anshulrose2
 
PEMDAS - The Proper Order of Mathematical Operations
PEMDAS - The Proper Order of Mathematical OperationsPEMDAS - The Proper Order of Mathematical Operations
PEMDAS - The Proper Order of Mathematical Operations
Mark (Mong) Montances
 
Solid Figures
Solid FiguresSolid Figures
Solid Figures
Lea Perez
 
Triangle and its properties
Triangle and its propertiesTriangle and its properties
Triangle and its properties
yas5
 
Elapsed Time
Elapsed TimeElapsed Time
Elapsed Timeemteacher
 
Addition and subtraction expressions
Addition and subtraction expressionsAddition and subtraction expressions
Addition and subtraction expressionsamccasland
 
Grade 2 PPT_MTB_Q1_File 10.pptx
Grade 2 PPT_MTB_Q1_File 10.pptxGrade 2 PPT_MTB_Q1_File 10.pptx
Grade 2 PPT_MTB_Q1_File 10.pptx
docilyn eslava
 
Rounding Decimals
Rounding DecimalsRounding Decimals
Rounding Decimals
anngorsuch
 
What's hot (20)

2D and 3D shapes and describe their properties ppt.pptx
2D and 3D shapes and describe their properties ppt.pptx2D and 3D shapes and describe their properties ppt.pptx
2D and 3D shapes and describe their properties ppt.pptx
 
Calculating speed time and distance
Calculating speed time and distanceCalculating speed time and distance
Calculating speed time and distance
 
Integers Class 7
Integers Class 7 Integers Class 7
Integers Class 7
 
Lines and angles
Lines and anglesLines and angles
Lines and angles
 
Area of a triangle
Area of a triangleArea of a triangle
Area of a triangle
 
Frequency tables and line plots
Frequency tables and line plotsFrequency tables and line plots
Frequency tables and line plots
 
Square Roots And Perfect Squares
Square Roots And Perfect SquaresSquare Roots And Perfect Squares
Square Roots And Perfect Squares
 
Visualising solid shapes
Visualising solid shapesVisualising solid shapes
Visualising solid shapes
 
Enlargements
EnlargementsEnlargements
Enlargements
 
Area of rectangles
Area of rectanglesArea of rectangles
Area of rectangles
 
Area of quadrilaterals
Area of quadrilateralsArea of quadrilaterals
Area of quadrilaterals
 
triangle and its properties
triangle and its propertiestriangle and its properties
triangle and its properties
 
PEMDAS - The Proper Order of Mathematical Operations
PEMDAS - The Proper Order of Mathematical OperationsPEMDAS - The Proper Order of Mathematical Operations
PEMDAS - The Proper Order of Mathematical Operations
 
Solid Figures
Solid FiguresSolid Figures
Solid Figures
 
Properties of 3 d shapes
Properties of 3 d shapesProperties of 3 d shapes
Properties of 3 d shapes
 
Triangle and its properties
Triangle and its propertiesTriangle and its properties
Triangle and its properties
 
Elapsed Time
Elapsed TimeElapsed Time
Elapsed Time
 
Addition and subtraction expressions
Addition and subtraction expressionsAddition and subtraction expressions
Addition and subtraction expressions
 
Grade 2 PPT_MTB_Q1_File 10.pptx
Grade 2 PPT_MTB_Q1_File 10.pptxGrade 2 PPT_MTB_Q1_File 10.pptx
Grade 2 PPT_MTB_Q1_File 10.pptx
 
Rounding Decimals
Rounding DecimalsRounding Decimals
Rounding Decimals
 
Recently uploaded

النزاع-ا لعرقي-والقبلي-في-دولة-جنوب-السودان-وانعكاساته-على-بناء-الدولة-4.pdf
النزاع-ا   لعرقي-والقبلي-في-دولة-جنوب-السودان-وانعكاساته-على-بناء-الدولة-4.pdfالنزاع-ا   لعرقي-والقبلي-في-دولة-جنوب-السودان-وانعكاساته-على-بناء-الدولة-4.pdf
النزاع-ا لعرقي-والقبلي-في-دولة-جنوب-السودان-وانعكاساته-على-بناء-الدولة-4.pdf
Gamal Mansour
 
Ingresantes en el examen general unap 2023 I.pdf
Ingresantes en el examen general unap 2023 I.pdfIngresantes en el examen general unap 2023 I.pdf
Ingresantes en el examen general unap 2023 I.pdf
wilfacemeet
 
HVAC 1 التدفئة والتهوية و تكييف الهواء
HVAC  1 التدفئة والتهوية  و تكييف الهواءHVAC  1 التدفئة والتهوية  و تكييف الهواء
HVAC 1 التدفئة والتهوية و تكييف الهواء
maymohamed29
 
guia informatica Guanajuato modulo 22 nuples
guia informatica Guanajuato modulo 22 nuplesguia informatica Guanajuato modulo 22 nuples
guia informatica Guanajuato modulo 22 nuples
Examenes Preparatoria Abierta
 
Panduan Pelaksanaan KCJ .pdf Kementerian Pendidikan Malaysia
Panduan Pelaksanaan KCJ .pdf Kementerian Pendidikan MalaysiaPanduan Pelaksanaan KCJ .pdf Kementerian Pendidikan Malaysia
Panduan Pelaksanaan KCJ .pdf Kementerian Pendidikan Malaysia
NORHAWABINTIAHMADAHS
 
أفضل 11 موقع لعمل اختبارات إلكترونية (Slide Decks).pdf
أفضل 11 موقع لعمل اختبارات إلكترونية (Slide Decks).pdfأفضل 11 موقع لعمل اختبارات إلكترونية (Slide Decks).pdf
أفضل 11 موقع لعمل اختبارات إلكترونية (Slide Decks).pdf
qorrectdm
 
Recently uploaded (6)

  • 2. Kukhala mchitantchito (mwininkhani) • Dzina limakhala mchitantchito ngati likugwira ntchito m’chiganizo. Zitsanzo • Madalitso akuyendetsa galimoto. • Abambo akulima.
  • 3. Kukhala mchitidwantchito (pamtherankhani) • Dzina limakhala mchitidwantchito ngati ntchito yachitikira pa ilo m’chiganizo. Mayina omwe amakhala mchitidwantchito amagwira ntchito zitatu zomwe ndi kukhala mchitidwantchito wa chindunji, wopanda chindunji ndi wamperekezi.
  • 4. (a) Kukhala mchitidwantchito wachindunji • Dzina limakhala mchitidwantchito wachindunji pamene ntchito ya mneni yachitikira pa ilo molunjika. Zitsanzo • Mphatso akumweta udzu. • Tikudya bwemba. • Nasibeko waumba mphika.
  • 5. (b) Kukhala mchitidwantchito wopanda chindunji • Dzina limakhala mchitidwantchito wopanda chindunji pamene ntchito ya mneni siinachitike pa ilo molunjika koma langokhudzidwa chabe ndi ntchitoyo. Zitsanzo • Maliya walembera agogo kalata. • Mphatso wagulira Mwayi pensulo.
  • 6. (c) Kukhala mchitidwantchito wa mperekezi • Dzina limakhala mchitidwantchito wa mperekezi pamene lili patsogolo pa mperekezi m’chiganizo. Zitsanzo • Wandicheka ndi mpeni. • Wapita kwa amalume.
  • 7. Kukhala mtsirizitsi wa tanthauzo la mneni • Dzina limakhala mtsirizitsi wa tanthauzo la mneni pamene likumalizitsa tanthauzo la mneni kuti limveke bwino m’chiganizo. Zitsanzo • Mphunzitsiyo ndi katswiri. • M’kalasi muli ophunzira ochepa.
  • 8. Kukhala dzina loitanira • Dzina limakhala loitanira pamene likusonyeza za yemwe akuitanidwa pa nthawiyo. Zitsanzo • Chifundo, bwera kuno. • Ananu, pitani kunyumba