SlideShare a Scribd company logo
Ntchito za zizindikiro
zam’kalembedwe
Mpumiro (.)
• Chizindikirochi chimagwira ntchito
zosiyanasiyana motere:
• kusonyeza kupuma pothera chiganizo.
• Zitsanzo
• Ana akusewera pamchenga.
• Azakhali aphika thobwa lokoma.
Ntchito ya mpumiro kupitilira…
• kusonyeza chidule cha mayina
• Zitsanzo
• Mayi B.A. Dzonzi asamukira ku Lilongwe.
• Ndimagwira ntchito ku M.C.D.E.
Mpatuliro (,)
• Chizindikirochi chimagwira ntchito zingapo
motere:
kusonyeza kupuma pang’ono pamene
mukuwerenga
• Zitsanzo
• Mphatso atalephera mayeso, adayamba
kuwerenga kwambiri.
• Zinthu zikakuvuta, sibwino kutaya mtima.
Ntchito za mpatuliro, kupitilira…..
• kupatula zinthu zomwe zili mu mndandanda.
• Zitsanzo
• Atate agula njinga, malata ndi nsapato.
• Aphunzitsi, makolo ndi ophunzira asonkhana.
Ntchito za mpatuliro, kupitilira…
• kusonyezanso dzina loitanira.
Zitsanzo
• Nabetha, bweretsa mwanayo.
• Bwana, ndipatseni katundu uja.
Mfunsiro (?)
• Chizindikirochi chimasonyeza kufunsa.
Zitsanzo
• Kodi mudzabwera liti?
• Muli bwanji?
• Chifukwa chiyani mwachedwa?
Mfuwuliro (!)
• Chizindikirochi chimasonyeza kuyankhula
mofuwula munthu akakondwa, akadabwa,
akadandaula kapena kunyansidwa.
Zitsanzo
• Mayo! Galu wandiluma.
• Hehede! Ndakhoza mayeso.
• Oo! Wadya yekha mpunga uja.
Nkhodolero (‘)
• Chizindikirochi chimagwira ntchito izi:
• kusonyeza kuti lembo lina lasiyidwa pofuna
kufupikitsa mawu.
Zitsanzo
• Ndam’dyera nsima yake.
• Tidam’patsa malaya a mwana wanga
Ntchito za nkhodolero kupitilira….
• Kufuna kutchula bwino mawu osonyeza malo
Zitsanzo
Munyumba – m’nyumba
Mumwamba – m’mwamba
Mumadzi – m’madzi
Ntchito za nkhodolero kupitilira….
• kusonyeza phatikizo la madzeramphuno.
Potchula mawu, mpweyaumatulukira
m’mphuno
• chitsanzo: ng’, m’mawu awa: ng’ala, ng’ona,
ng’oma, kang’wing’wi, ng’amba.
Mdulamawu (-)
• Chizindikirochi chimasonyeza kudula mawu
omwe apitirira mzere pamene mukulemba.
Muzidulapothera phatikizo ndi poyambira
phatikizo,osati pa lembo la mtsekanjira koma
la mtsekulanjira.

More Related Content

What's hot

SIYINI ISENZO
SIYINI ISENZOSIYINI ISENZO
SIYINI ISENZO
Bongumenzi Mtshali
 
Ubuciko bomlomo
Ubuciko bomlomoUbuciko bomlomo
Сэтгэх чадвар
Сэтгэх чадварСэтгэх чадвар
Сэтгэх чадвар
Erdenejargal Narantuya
 
Ulimi lwesizulu ulimi lwasekhaya
Ulimi lwesizulu ulimi lwasekhayaUlimi lwesizulu ulimi lwasekhaya
Ulimi lwesizulu ulimi lwasekhaya
University of johannesburg
 
математик 6-р анги "Координатын систем"
математик 6-р анги "Координатын систем"математик 6-р анги "Координатын систем"
математик 6-р анги "Координатын систем"
tsbmb
 
цахим хичээл
цахим хичээлцахим хичээл
цахим хичээлouyha
 
UBUCIKO BOMLOMO
UBUCIKO BOMLOMOUBUCIKO BOMLOMO
лого тэмдгийн байгуулалт
лого тэмдгийн байгуулалтлого тэмдгийн байгуулалт
лого тэмдгийн байгуулалтburam_l
 
D. tumen ulzii tsahim uzuulen
D. tumen ulzii tsahim uzuulenD. tumen ulzii tsahim uzuulen
D. tumen ulzii tsahim uzuulenolzii555
 
Izindlela zesenzo (2)
Izindlela zesenzo (2)Izindlela zesenzo (2)
Izindlela zesenzo (2)
vivian khanye
 
5 р ангийн монгол хэлний тест 8
5 р ангийн монгол хэлний тест 85 р ангийн монгол хэлний тест 8
5 р ангийн монгол хэлний тест 8shiirev2905
 
Sakhiwo selibito
Sakhiwo selibitoSakhiwo selibito
Sakhiwo selibito
MachaweDlamini1
 
Цахим хичээл
Цахим хичээлЦахим хичээл
Цахим хичээлTseegii Nandia
 
Izindlela zesenzo tst3 b
Izindlela zesenzo tst3 bIzindlela zesenzo tst3 b
Izindlela zesenzo tst3 b
Colile Dlamini
 
7в ангийн сэтгэл ханамжийн судалгаа
7в ангийн сэтгэл ханамжийн судалгаа 7в ангийн сэтгэл ханамжийн судалгаа
7в ангийн сэтгэл ханамжийн судалгаа gantuya35
 

What's hot (16)

SIYINI ISENZO
SIYINI ISENZOSIYINI ISENZO
SIYINI ISENZO
 
Ubuciko bomlomo
Ubuciko bomlomoUbuciko bomlomo
Ubuciko bomlomo
 
IsiZulu
IsiZulu IsiZulu
IsiZulu
 
Сэтгэх чадвар
Сэтгэх чадварСэтгэх чадвар
Сэтгэх чадвар
 
Ulimi lwesizulu ulimi lwasekhaya
Ulimi lwesizulu ulimi lwasekhayaUlimi lwesizulu ulimi lwasekhaya
Ulimi lwesizulu ulimi lwasekhaya
 
математик 6-р анги "Координатын систем"
математик 6-р анги "Координатын систем"математик 6-р анги "Координатын систем"
математик 6-р анги "Координатын систем"
 
цахим хичээл
цахим хичээлцахим хичээл
цахим хичээл
 
UBUCIKO BOMLOMO
UBUCIKO BOMLOMOUBUCIKO BOMLOMO
UBUCIKO BOMLOMO
 
лого тэмдгийн байгуулалт
лого тэмдгийн байгуулалтлого тэмдгийн байгуулалт
лого тэмдгийн байгуулалт
 
D. tumen ulzii tsahim uzuulen
D. tumen ulzii tsahim uzuulenD. tumen ulzii tsahim uzuulen
D. tumen ulzii tsahim uzuulen
 
Izindlela zesenzo (2)
Izindlela zesenzo (2)Izindlela zesenzo (2)
Izindlela zesenzo (2)
 
5 р ангийн монгол хэлний тест 8
5 р ангийн монгол хэлний тест 85 р ангийн монгол хэлний тест 8
5 р ангийн монгол хэлний тест 8
 
Sakhiwo selibito
Sakhiwo selibitoSakhiwo selibito
Sakhiwo selibito
 
Цахим хичээл
Цахим хичээлЦахим хичээл
Цахим хичээл
 
Izindlela zesenzo tst3 b
Izindlela zesenzo tst3 bIzindlela zesenzo tst3 b
Izindlela zesenzo tst3 b
 
7в ангийн сэтгэл ханамжийн судалгаа
7в ангийн сэтгэл ханамжийн судалгаа 7в ангийн сэтгэл ханамжийн судалгаа
7в ангийн сэтгэл ханамжийн судалгаа
 

Zizindikiro za m'kalembedwe

  • 2. Mpumiro (.) • Chizindikirochi chimagwira ntchito zosiyanasiyana motere: • kusonyeza kupuma pothera chiganizo. • Zitsanzo • Ana akusewera pamchenga. • Azakhali aphika thobwa lokoma.
  • 3. Ntchito ya mpumiro kupitilira… • kusonyeza chidule cha mayina • Zitsanzo • Mayi B.A. Dzonzi asamukira ku Lilongwe. • Ndimagwira ntchito ku M.C.D.E.
  • 4. Mpatuliro (,) • Chizindikirochi chimagwira ntchito zingapo motere: kusonyeza kupuma pang’ono pamene mukuwerenga • Zitsanzo • Mphatso atalephera mayeso, adayamba kuwerenga kwambiri. • Zinthu zikakuvuta, sibwino kutaya mtima.
  • 5. Ntchito za mpatuliro, kupitilira….. • kupatula zinthu zomwe zili mu mndandanda. • Zitsanzo • Atate agula njinga, malata ndi nsapato. • Aphunzitsi, makolo ndi ophunzira asonkhana.
  • 6. Ntchito za mpatuliro, kupitilira… • kusonyezanso dzina loitanira. Zitsanzo • Nabetha, bweretsa mwanayo. • Bwana, ndipatseni katundu uja.
  • 7. Mfunsiro (?) • Chizindikirochi chimasonyeza kufunsa. Zitsanzo • Kodi mudzabwera liti? • Muli bwanji? • Chifukwa chiyani mwachedwa?
  • 8. Mfuwuliro (!) • Chizindikirochi chimasonyeza kuyankhula mofuwula munthu akakondwa, akadabwa, akadandaula kapena kunyansidwa. Zitsanzo • Mayo! Galu wandiluma. • Hehede! Ndakhoza mayeso. • Oo! Wadya yekha mpunga uja.
  • 9. Nkhodolero (‘) • Chizindikirochi chimagwira ntchito izi: • kusonyeza kuti lembo lina lasiyidwa pofuna kufupikitsa mawu. Zitsanzo • Ndam’dyera nsima yake. • Tidam’patsa malaya a mwana wanga
  • 10. Ntchito za nkhodolero kupitilira…. • Kufuna kutchula bwino mawu osonyeza malo Zitsanzo Munyumba – m’nyumba Mumwamba – m’mwamba Mumadzi – m’madzi
  • 11. Ntchito za nkhodolero kupitilira…. • kusonyeza phatikizo la madzeramphuno. Potchula mawu, mpweyaumatulukira m’mphuno • chitsanzo: ng’, m’mawu awa: ng’ala, ng’ona, ng’oma, kang’wing’wi, ng’amba.
  • 12. Mdulamawu (-) • Chizindikirochi chimasonyeza kudula mawu omwe apitirira mzere pamene mukulemba. Muzidulapothera phatikizo ndi poyambira phatikizo,osati pa lembo la mtsekanjira koma la mtsekulanjira.