Mitundu ya alowammalo
- 4. Mlowam’malo wa dzina lakelake
• Mlowam’malo uyu amagwiritsidwa ntchito
m’malo mwa dzina la munthu. Alowam’malowa
alipo a mitundu itatu motere:
• Mlowam’malo wakalozamwini
• Uyu amaimira dzina la munthu kapena anthu
amene akuyankhula.
Zitsanzo
• (i) Ine ndikhoza mayeso.
• (ii) Ife takondwa kwambiri.
- 5. Mlowammalo wa dzina lakelake
kupitilira
• Mlowam’malo wakalozamnzako
• Uyu amaimira dzina la munthu yemwe
akutchulidwa ndipo akudzimvera zomwe
zikunenedwa.
• Zitsanzo
• (i) Iwe, tenga nkhukuyi.
• (ii) Inu, tsatirani anzanuwo
- 6. Mlowam’malo wakalozamnzako
• Uyu amaimira dzina la munthu yemwe
akutchulidwa ndipo akudzimvera zomwe
zikunenedwa.
• Zitsanzo
• (i) Iwe, tenga nkhukuyi.
• (ii) Inu, tsatirani anzanuwo